
English
History & religion
Limited Offer
Then 99 kr. / monthCancel anytime.
About Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa
Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera pologalamu imodzi patsiku kuyambira lolemba mpaka lachisanu. Ngati mungakwanitse kutsatira ndondomekoyi, pakutha kwa zaka zisanu mudzakhala kuti mwawerenga Baibulo lonse.
489 episodes
Chitsimikizo cha chipulumutso chathu.
Chitsimikizo cha chipulumutso chathu
Wokhulupirira ayenera kulilaka/kugonjetsa dziko lapansi
Mulungu ndiye moyo
Wokhulupirira ayenera kukondana wina ndi mnzake
Choose your subscription
Most popular
Limited Offer
Premium
20 hours of audiobooks
Podcasts only on Podimo
No ads in Podimo shows
Cancel anytime
1 month for 9 kr.
Then 99 kr. / month
Premium Plus
Unlimited audiobooks
Podcasts only on Podimo
No ads in Podimo shows
Cancel anytime
Start 7 days free trial
Then 129 kr. / month
1 month for 9 kr. Then 99 kr. / month. Cancel anytime.